Nzika yaku Nigeria yagwidwa ndi cocaine
Advertisement Apolisi m’boma wa Lilongwe amanga nzika ya m’dziko la Nigeria yazaka 43 kamba kopezeka ndi timaphukusi 33 ta mankhwala ozunguza ubongo a cocaine. Malingana ndi wachiwiri kwa ofalitsa za polisi mchigawo cha kumadzulo mchigawo chapakati a …